-
2 Mafumu 3:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Aisiraeli anayamba kugwetsa mizinda. Pamalo alionse abwino, aliyense anali kuponyapo mwala mpaka kudzaza malo onsewo. Anatseka kasupe aliyense wamadzi+ ndiponso kugwetsa mtengo uliwonse wabwino.+ Mpanda wamiyala wa mzinda wa Kiri-hareseti+ wokha ndi umene unatsala ndipo oponya miyala anazungulira mzindawo nʼkugwetsa mpandawo.
-