2 Mafumu 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Elisa anamuyankha kuti: “Ndiye ndikuchitire chiyani? Tandiuze, uli ndi chiyani mʼnyumba mwako?” Mayiyo anayankha kuti: “Ine kapolo wanu ndilibe chilichonse mʼnyumba mwanga, ndili ndi kamtsuko ka mafuta kokha basi.”+
2 Elisa anamuyankha kuti: “Ndiye ndikuchitire chiyani? Tandiuze, uli ndi chiyani mʼnyumba mwako?” Mayiyo anayankha kuti: “Ine kapolo wanu ndilibe chilichonse mʼnyumba mwanga, ndili ndi kamtsuko ka mafuta kokha basi.”+