-
2 Mafumu 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ukakatero, iwe ndi ana akowo mukalowe mʼnyumba nʼkutseka chitseko. Ndiyeno uzikathira mafutawo mʼzotengerazo. Zimene zadzaza uzikaziika pambali.”
-