2 Mafumu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza Elisa kuti adye chakudya.+ Nthawi zonse Elisa akamadutsa, ankaima kunyumba kwa mayiyo kuti adye chakudya.
8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza Elisa kuti adye chakudya.+ Nthawi zonse Elisa akamadutsa, ankaima kunyumba kwa mayiyo kuti adye chakudya.