2 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Kandiitanire mayi uja.”+ Choncho iye anamuitana ndipo anaima pamaso pa Elisa.
12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Kandiitanire mayi uja.”+ Choncho iye anamuitana ndipo anaima pamaso pa Elisa.