2 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mayiyo anatenga mwanayo nʼkukamugoneka pabedi la munthu wa Mulungu woona uja.+ Atatero anatuluka nʼkutseka chitseko.
21 Ndiyeno mayiyo anatenga mwanayo nʼkukamugoneka pabedi la munthu wa Mulungu woona uja.+ Atatero anatuluka nʼkutseka chitseko.