-
2 Mafumu 4:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndiyeno mayiyo atakwera bulu, anauza wantchito wake kuti: “Buluyu uzimuthamangitsa, usayende pangʼonopangʼono chifukwa cha ine, pokhapokha ndikakuuza.”
-