-
2 Mafumu 4:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho mayiyo anapita kwa munthu wa Mulungu woona uja kuphiri la Karimeli. Munthu wa Mulunguyo atangoona mayiyo, anauza mtumiki wake Gehazi kuti: “Mayi wa ku Sunemu uja uyo! Akubwera.
-