2 Mafumu 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi kuti: “Manga zovala zako mʼchiuno.+ Tenga ndodo yangayi uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamʼpatse moni ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mnyamatayo.”
29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi kuti: “Manga zovala zako mʼchiuno.+ Tenga ndodo yangayi uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamʼpatse moni ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mnyamatayo.”