2 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma mayi wa mwanayo anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.”+ Choncho Elisa ananyamuka nʼkupita limodzi ndi mayiyo.
30 Koma mayi wa mwanayo anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.”+ Choncho Elisa ananyamuka nʼkupita limodzi ndi mayiyo.