2 Mafumu 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako anapita pabedipo ndipo anagwada nʼkuweramira mwanayo. Anagunditsa pakamwa pake ndi pakamwa pa mwanayo, maso ake ndi maso a mwanayo komanso manja ake ndi manja a mwanayo. Anakhalabe choncho mpaka thupi la mwanayo linayamba kutentha.+
34 Kenako anapita pabedipo ndipo anagwada nʼkuweramira mwanayo. Anagunditsa pakamwa pake ndi pakamwa pa mwanayo, maso ake ndi maso a mwanayo komanso manja ake ndi manja a mwanayo. Anakhalabe choncho mpaka thupi la mwanayo linayamba kutentha.+