2 Mafumu 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako anayamba kuyenda uku ndi uku mʼnyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Ndiyeno mwanayo anayetsemula maulendo 7, kenako anayamba kuyangʼana.+
35 Kenako anayamba kuyenda uku ndi uku mʼnyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Ndiyeno mwanayo anayetsemula maulendo 7, kenako anayamba kuyangʼana.+