2 Mafumu 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Elisa anabwerera ku Giligala ndipo kunali njala.+ Ndiyeno ana a aneneri+ anabwera kwa iye nʼkukhala pansi. Elisa anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”
38 Kenako Elisa anabwerera ku Giligala ndipo kunali njala.+ Ndiyeno ana a aneneri+ anabwera kwa iye nʼkukhala pansi. Elisa anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”