-
2 Mafumu 4:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Mmodzi wa ana aneneriwo anapita kutchire kukathyola masamba. Iye anapezako kamtengo koyanga ka mphonda zakutchire ndipo anathyolapo mphonda zodzaza pachovala chake. Atabwera nazo anaziduladula nʼkuziika mumphika muja koma sankazidziwa bwinobwino.
-