2 Mafumu 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno Elisa anati: “Bweretsani ufa.” Atathira ufawo mumphikamo, ananena kuti: “Apatseni anthuwa kuti adye.” Atatero, mumphikamo munalibenso poizoni.+
41 Ndiyeno Elisa anati: “Bweretsani ufa.” Atathira ufawo mumphikamo, ananena kuti: “Apatseni anthuwa kuti adye.” Atatero, mumphikamo munalibenso poizoni.+