2 Mafumu 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno kunabwera munthu wina kuchokera ku Baala-salisa.+ Iye anabweretsera munthu wa Mulungu woonayo mikate 20 ya balere+ woyambirira kucha komanso thumba la tirigu* watsopano.+ Kenako Elisa anati: “Apatse anthuwa kuti adye.”
42 Ndiyeno kunabwera munthu wina kuchokera ku Baala-salisa.+ Iye anabweretsera munthu wa Mulungu woonayo mikate 20 ya balere+ woyambirira kucha komanso thumba la tirigu* watsopano.+ Kenako Elisa anati: “Apatse anthuwa kuti adye.”