2 Mafumu 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma mtumiki wakeyo anati: “Ndingagawire bwanji anthu 100 chakudya chimenechi?”+ Elisa anati: “Agawire anthuwa kuti adye chifukwa Yehova wanena kuti, ‘Anthu adya nʼkukhuta ndipo china chitsala.’”+
43 Koma mtumiki wakeyo anati: “Ndingagawire bwanji anthu 100 chakudya chimenechi?”+ Elisa anati: “Agawire anthuwa kuti adye chifukwa Yehova wanena kuti, ‘Anthu adya nʼkukhuta ndipo china chitsala.’”+