8 Koma Elisa, munthu wa Mulungu woona, atamva kuti mfumu ya Isiraeli yangʼamba zovala zake, nthawi yomweyo anatumiza uthenga kwa mfumuyo wakuti: “Nʼchifukwa chiyani mwangʼamba zovala zanu? Muuzeni abwere kuno kuti adziwe kuti ku Isiraeli kuli mneneri.”+