2 Mafumu 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Elisa anatuma munthu kukamuuza kuti: “Pitani mukasambe maulendo 7+ mumtsinje wa Yorodano+ ndipo thupi lanu libwerera mwakale ndipo mukhala woyera.”
10 Koma Elisa anatuma munthu kukamuuza kuti: “Pitani mukasambe maulendo 7+ mumtsinje wa Yorodano+ ndipo thupi lanu libwerera mwakale ndipo mukhala woyera.”