-
2 Mafumu 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma atumiki ake anamutsatira nʼkumufunsa kuti: “Bambo wanga, kodi mneneriyo akanakuuzani kuti muchite chinthu chachikulu, simukanachita? Nanga bwanji poti wangokuuzani kuti, ‘Kasambeni ndipo mukhala woyeraʼ?”
-