-
2 Mafumu 6:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Munthu wina akudula mtengo, nkhwangwa inaguluka nʼkugwera mʼmadzi. Zitatero munthuyo anafuula kuti: “Mayo ine! Nkhwangwayi inali yobwereka!”
-