-
2 Mafumu 6:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Munthu wa Mulungu woonayo anafunsa kuti: “Yagwera pati?” Iye anamusonyeza pamene inagwera. Elisa anadula kamtengo nʼkukaponya pamene inagwerapo ndipo nkhwangwayo inayandama.
-