-
2 Mafumu 6:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mtumiki wa munthu wa Mulungu woona atadzuka mʼmawa nʼkutuluka panja, anaona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anauza mbuye wake kuti: “Mayo ine mbuyanga! Titani?”
-