2 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Elisa anati: “Musawaphe. Kodi mukufuna kupha anthu amene mwawagonjetsa ndi lupanga ndi uta nʼkuwagwira? Apatseni chakudya ndi madzi kuti adye ndi kumwa.+ Kenako azipita kwa mbuye wawo.”
22 Koma Elisa anati: “Musawaphe. Kodi mukufuna kupha anthu amene mwawagonjetsa ndi lupanga ndi uta nʼkuwagwira? Apatseni chakudya ndi madzi kuti adye ndi kumwa.+ Kenako azipita kwa mbuye wawo.”