2 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anadya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba a ku Siriya+ sanabwerenso ku Isiraeli.
23 Choncho mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anadya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba a ku Siriya+ sanabwerenso ku Isiraeli.