2 Mafumu 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho mu Samariya munagwa njala yaikulu.+ Asiriyawo anapitirizabe kuzungulira mzindawo mpaka mtengo wogulira mutu wa bulu+ unafika pa ndalama 80 zasiliva ndipo zitosi za nkhunda zodzaza manja awiri* mtengo wake unali ndalama 5 zasiliva. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2139
25 Choncho mu Samariya munagwa njala yaikulu.+ Asiriyawo anapitirizabe kuzungulira mzindawo mpaka mtengo wogulira mutu wa bulu+ unafika pa ndalama 80 zasiliva ndipo zitosi za nkhunda zodzaza manja awiri* mtengo wake unali ndalama 5 zasiliva.