2 Mafumu 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno mfumuyo inamʼfunsa kuti: “Chavuta nʼchiyani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero ndipo mawa tidzadya mwana wanga.’+
28 Ndiyeno mfumuyo inamʼfunsa kuti: “Chavuta nʼchiyani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero ndipo mawa tidzadya mwana wanga.’+