2 Mafumu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho tinaphika mwana wanga nʼkumudya.+ Tsiku lotsatira ndinauza mayiyu kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye.’ Koma iye anakamʼbisa.”
29 Choncho tinaphika mwana wanga nʼkumudya.+ Tsiku lotsatira ndinauza mayiyu kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye.’ Koma iye anakamʼbisa.”