-
2 Mafumu 6:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Elisa anali mʼnyumba mwake pamodzi ndi akulu. Mfumu inatumiza munthu kuti atsogole kupita kwa Elisa, koma munthuyo asanafike Elisa anauza akuluwo kuti: “Kodi mwaona kuti mwana wa munthu wopha anthu+ uja watumiza munthu kuti adzandidule mutu? Muonetsetse kuti munthuyo akangofika mutseke chitseko ndipo muchitsamire kuti asalowe. Kodi mapazi a mbuye wake si amene akumveka pambuyo pakewo?”
-