-
2 Mafumu 6:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Elisa ali mkati molankhula nawo, munthu uja anafika ndipo mfumu inati: “Tsokali lachokera kwa Yehova. Kodi pali chifukwa choti ndipitirizire kuyembekezera Yehova?”
-