7 Elisa anati: “Mverani mawu a Yehova. Yehova wanena kuti, ‘Mawa nthawi ngati ino, pageti la Samariya ufa wosalala wokwana muyezo umodzi wa seya, mtengo wake udzakhala sekeli limodzi ndipo balere wokwana miyezo iwiri ya seya, mtengo wake udzakhalanso sekeli limodzi.’”+