-
2 Mafumu 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nthawi yomweyo asilikaliwo ananyamuka nʼkuyamba kuthawa kukungoyamba kumene kuda. Anasiya mahema awo, mahatchi awo komanso abulu awo. Msasawo anausiya mmene unalili nʼkuthawa kuti apulumutse moyo wawo.
-