-
2 Mafumu 7:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Anthuwo anatsatira Asiriyawo mpaka kukafika ku Yorodano ndipo mʼnjira monse munali zovala ndi ziwiya zimene Asiriyawo anataya pamene ankathawa mwamantha. Kenako anthuwo anabwerera nʼkukanena kwa mfumu.
-