-
2 Mafumu 7:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mfumu inaika msilikali woithandiza amene inkamudalira uja kuti aziyangʼanira pageti. Koma anthu anamʼpondaponda pagetipo moti anafa, mogwirizana ndi zimene munthu wa Mulungu woona uja ananena, pamene mfumu inapita kwa iye.
-