18 Zinachitikadi ngati mmene munthu wa Mulungu woona uja anauzira mfumu, kuti: “Balere wokwana miyezo iwiri ya seya mtengo wake udzakhala sekeli imodzi ndipo ufa wosalala wokwana muyezo umodzi wa seya, mtengo wake udzakhalanso sekeli imodzi mawa, nthawi ngati ino pageti la Samariya.”+