2 Mafumu 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana+ uja, kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale mlendo kulikonse kumene ungasankhe, chifukwa Yehova wanena kuti mʼdzikoli mudzakhala njala+ kwa zaka 7.”
8 Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana+ uja, kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale mlendo kulikonse kumene ungasankhe, chifukwa Yehova wanena kuti mʼdzikoli mudzakhala njala+ kwa zaka 7.”