-
2 Mafumu 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno mfumuyo inapempha mayiyo kuti afotokoze nkhani yonse ndipo mayiyo anafotokozadi. Kenako mfumuyo inauza nduna ya panyumba yake kuti: “Mayiyu umʼbwezere zinthu zake zonse komanso umupatse ndalama zimene akanapeza pa zokolola za kumunda kwake kuyambira pamene anachoka mpaka lero.”
-