2 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Elisa anapita ku Damasiko+ ndipo pa nthawiyo nʼkuti Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya akudwala. Choncho mfumuyo inauzidwa kuti: “Munthu wa Mulungu woona+ uja wabwera kuno.”
7 Kenako Elisa anapita ku Damasiko+ ndipo pa nthawiyo nʼkuti Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya akudwala. Choncho mfumuyo inauzidwa kuti: “Munthu wa Mulungu woona+ uja wabwera kuno.”