2 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli+ kuti: “Tenga mphatso ndipo upite kwa munthu wa Mulungu woonayo.+ Ukafunse kwa Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”
8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli+ kuti: “Tenga mphatso ndipo upite kwa munthu wa Mulungu woonayo.+ Ukafunse kwa Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”