2 Mafumu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hazaeli atamva mawu amenewa, anati: “Zingatheke bwanji kuti ine mtumiki wanu, galu ngati ine, ndichite zinthu ngati zimenezi?” Koma Elisa anati: “Yehova wandionetsa kuti iweyo udzakhala mfumu ya Siriya.”+
13 Hazaeli atamva mawu amenewa, anati: “Zingatheke bwanji kuti ine mtumiki wanu, galu ngati ine, ndichite zinthu ngati zimenezi?” Koma Elisa anati: “Yehova wandionetsa kuti iweyo udzakhala mfumu ya Siriya.”+