2 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda nʼkuchiviika mʼmadzi kenako anaphimba mfumuyo kumaso mpaka inamwalira.+ Ndiyeno Hazaeli anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+
15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda nʼkuchiviika mʼmadzi kenako anaphimba mfumuyo kumaso mpaka inamwalira.+ Ndiyeno Hazaeli anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+