2 Mafumu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anayenda mʼnjira ya mafumu a Isiraeli+ ngati mmene anachitira anthu a mʼbanja la Ahabu,+ chifukwa anakwatira mwana wa Ahabu.+ Ndipo iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+
18 Iye anayenda mʼnjira ya mafumu a Isiraeli+ ngati mmene anachitira anthu a mʼbanja la Ahabu,+ chifukwa anakwatira mwana wa Ahabu.+ Ndipo iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+