-
2 Mafumu 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Yehoramu anapita ku Zairi pamodzi ndi magaleta ake onse. Kumeneko, iye ananyamuka usiku nʼkukapha Aedomu amene anamuzungulira. Anaphanso atsogoleri a asilikali okwera magaleta ndipo asilikali ena onse anathawira kumatenti awo.
-