2 Mafumu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yehoramu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
24 Kenako Yehoramu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Kenako mwana wake Ahaziya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.