2 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayenda mʼnjira ya anthu a mʼbanja la Ahabu+ ndipo anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira anthu a mʼbanja la Ahabuwo, chifukwa anali wachibale wawo.+
27 Iye anayenda mʼnjira ya anthu a mʼbanja la Ahabu+ ndipo anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira anthu a mʼbanja la Ahabuwo, chifukwa anali wachibale wawo.+