2 Mafumu 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho iye anapita ku nkhondo ndi Yehoramu mwana wa Ahabu kukamenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Koma Asiriyawo anavulaza Yehoramu.+
28 Choncho iye anapita ku nkhondo ndi Yehoramu mwana wa Ahabu kukamenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Koma Asiriyawo anavulaza Yehoramu.+