2 Mafumu 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana a aneneri nʼkumuuza kuti: “Manga zovala zako mʼchiuno, nyamula botolo ladothi la mafutali ndipo upite mwamsanga ku Ramoti-giliyadi.+
9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana a aneneri nʼkumuuza kuti: “Manga zovala zako mʼchiuno, nyamula botolo ladothi la mafutali ndipo upite mwamsanga ku Ramoti-giliyadi.+