2 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukakafika mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukamupeza ali ndi abale ake ndipo ukamutenge nʼkulowa naye mʼchipinda chamkati.
2 Ukakafika mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukamupeza ali ndi abale ake ndipo ukamutenge nʼkulowa naye mʼchipinda chamkati.