2 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali nʼkumuthira pamutu ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli.”’+ Ukakatero, ukatsegule chitseko nʼkuthawa, usakachedwe.”
3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali nʼkumuthira pamutu ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli.”’+ Ukakatero, ukatsegule chitseko nʼkuthawa, usakachedwe.”