-
2 Mafumu 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yehu atabwerera kwa atumiki a mbuye wake, atumikiwo anamufunsa kuti: “Zili bwino kodi? Nanga munthu wamisalayu amadzatani?” Iye anawayankha kuti: “Inu mukumudziwa munthuyu ndiponso zonena zake.”
-